Nathan Chikoya - Sindiyenera lyrics
rate meSindinyenera Ambuya anga mulowe muno mwanga
Komatu mungo nena mau kundiciritsatu.
Kundiciritsatu, Kundiciritsatu
Kundiciritsa, Kundiciritsatu.
Sindinyenera Ambuye Yesu ndikala ngati bwinja
Mukhoza bwanji kulowamo kundiciritsatu.
Sindiyenera mwanankosa komanso mwandifera
Nimudawaza mwadzi wanu kundiciritsatu.
Ndiyamike bwanji Ambuya anga paumoyo mwandipatsa?
Ndimpatso bwanji ndipereke pazonse mwazicita?
Chifukwa mau anga safikapo ndimpatso yalepera!!!
Chakudya chanu Ambuye anga ndifuna kulandira
Mukale mphamvu mkati mwanga kundiciritsatu.
Mukale mphamvu mkati mwanga kundiciritsa he!he!!
[Credits: Public Domain recorded on 22nd July10
Bridge, alternative lyrics and tune by Nathan Chikoya
Public Notice: All rights reserved.
Print only for musical research and church use.]