Nathan Chikoya - Limbikira lyrics
rate meThis song is for every one whos going through a struggle Limbikira..
Pamene Atate anga anatisiya ndinaona monga dziko landitera.
Koma Amai analimbika kutisunga sanasiye kundilimbitsa,
Mwana wanga ukonde sikulu usewenze ndimanja ako!!
Mwana wanga Limbikira mwana wanga umoyo ndinkondo,
Ukacita ulesi uzadya maudzu mwana wanga limbikira.
Mwana wanga Limbikira mwana wanga umoyo ndinkondo,
Ukacita ulesi uzadya maudzu mwana wanga limbikira.
Ndikakumbukira mau ya Amai ndimagwada ndiyamika Mulungu,
Pamau anu olimbitsa mau anu opatsa nzelu.
Ndipamene ndipedza zolimba zamudziko ndikumbukira mau anu akuti!!!
Yeah!! It doesn't feel so bad I was just like you
I used to wake up with no food just like you
I lost my daddy just like you
But that has got none to do with you men
All you have to do is hold on and be strong pray to God
He watches over you cause he will never leave your side, never leave your side!!!
[Words and music by Nathan Chikoya
Rap contribution by Alfred Redalf Chikoya
Written on 29th March09, recorded on 8th October09
© 2010 Nathan Chikoya
Public Notice: All rights reserved.
Print only for musical research and church use.]