MAGENTELE

MAGENTELE - Wha Wi Goin Crazy lyrics

rate me

(whiska)

(gentele)

CHORUS..

these gals pon mi mind

wha why wi goin crazy n crazy

these gals pon mi mind wha

why wi goin crazy...x2

verse 1..Z3X

yeah..

why wi..why wi..why wi going crazy

umadziwa akazi anatha axse/

koma kankazi aka kokha kali nyatwa axse/

ofunika kukagyniiza no mantha axse/

panopa sindichedwesanso ndingothatha axse/

zenizenizo tizipange axse/

wina aliyense wamwano ndimulanga axse/

ndikathatha kachikika kakhala kanga axse/

kazindichiza ndikadwala ngati pharmacy/

(Whisker man)

zoom..zoom nkazi ndipatse room/

ndiprophesyya ngati prophet of doom/

muworld yako nkazi ndikhala mfumu/

ndiwe osowa ngati verse m'bukhu la Nahum/ (oza!!!!!)

nkazi takhala paize/

ndikakuona dona ine ndimafila dizzy/

ndimakufila nkazi wina asakunamize/

sendera pafupi..ey..undikise/

CHORUS...

verse 2...

(Z3X)

iwe nkazi mvera zaGentele/

wangolowa mumtima mwanga kumenya chientele(entry)/

winaaliyense wansanje achenjere/

amangokhalira kumathoka amvekele/

zinthu zimuvute zimuswekele/

asowe kolowela ndithu timutsekele/

kufuna chikondi chaine chimveke mchere/

ndimangothawila kutali kumenya wentele«(Gentele's vocab)/

(Whisker man a.k.a Zepha)

amangothoka amangonena iwo amangodissa/

sipamadutsa minute inayo osakumissa/

missin..missin sindimadzipanga handle/

surely iweyo ndi ine tidzaphula scandal/

ndikuthoke zomwe mumtima zinabisika/

luv yanga plenty ngati anga mawhisker/

chix ndindani amagula pa msiska(msika)/

ine ndine Mr iwe ndiwe Miss K..A/

Chorus......

Thanks to Dacta Z3X

Thanks to Mbumba ya Abraham for correcting these lyrics

Get this song at:  amazon.com  sheetmusicplus.com

Share your thoughts

0 Comments found