Lidia Pospieszalska - Ndili bwino lyrics
rate meNdili bwino, ndakondwa
Ndikupita ku nyumba
Mudzi uli pafupi
Tsiku lonse, madzulo
Ndili bwino, ndakondwa
Ndikupita ku nyumba
Tauni uli pafupi
Monitu tso-o-no!
Kunyumba kuli bwanji?
Onse ali bwino?