David Kuthyola - Matamando lyrics
rate mendiimba matamando
popeza ndinu oyera
ndikhulupira inu
tate wa dziko lonse
chorus
wa zakumwamba ndi zapansi
ayenera matamando
ine ndikhulupila iye
tate wadziko lonse
ndiimba matamando
ndinu oyera mnjira zonse
inu mundiyang'anira
masiku amoyo wanga
back to chorus